-
Ezekieli 42:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kutsogolo kwa zipinda zodyeramozo kunali njira yofanana ndi ya zipinda zodyeramo za mbali ya kumpoto. M’litali ndi m’lifupi mwa zipindazo munali mofanana ndi mwa zipinda za kumpoto.+ Makomo otulukira a zipindazo, kamangidwe ka zipindazo ndiponso makomo ake olowera, zinali zofanana ndi zipinda za kumpoto zija.
-