Ezekieli 42:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakati pa zipinda zodyeramo panali njira yolowera mkati ya mikono 10 m’lifupi mwake.+ Panalinso kanjira ka mkono umodzi, kotuluka m’zipindazo kulowa m’njira ina ija. Makomo a zipindazo analoza mbali ya kumpoto.
4 Pakati pa zipinda zodyeramo panali njira yolowera mkati ya mikono 10 m’lifupi mwake.+ Panalinso kanjira ka mkono umodzi, kotuluka m’zipindazo kulowa m’njira ina ija. Makomo a zipindazo analoza mbali ya kumpoto.