Ekisodo 28:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Ana a Aroni uwapangire mikanjo+ ndi malamba ake. Uwapangirenso mipango*+ yokulunga kumutu kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+ Ekisodo 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ukatero utenge ana ake ndi kuwaveka mikanjo.+ Levitiko 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Mose anaitana ana a Aroni+ ndi kuwaveka mikanjo, kuwamanga malamba a pamimba,+ ndi kuwakulunga mipango+ kumutu, monga mmene Yehova analamulira Mose. Ezekieli 44:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Akafuna kupita kubwalo lakunja kumene kuli anthu, azivula zovala zawo zimene anavala potumikira.+ Aziika zovalazo m’zipinda zopatulika zodyeramo+ ndipo azivala zovala zina kuti asayeretse anthu ndi zovala zawozo.+
40 “Ana a Aroni uwapangire mikanjo+ ndi malamba ake. Uwapangirenso mipango*+ yokulunga kumutu kuti iwapatse ulemerero ndi kuwakongoletsa.+
13 Kenako Mose anaitana ana a Aroni+ ndi kuwaveka mikanjo, kuwamanga malamba a pamimba,+ ndi kuwakulunga mipango+ kumutu, monga mmene Yehova analamulira Mose.
19 Akafuna kupita kubwalo lakunja kumene kuli anthu, azivula zovala zawo zimene anavala potumikira.+ Aziika zovalazo m’zipinda zopatulika zodyeramo+ ndipo azivala zovala zina kuti asayeretse anthu ndi zovala zawozo.+