Ezekieli 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chipata choyang’ana kum’mawa cha bwalo lamkati+ chizikhala chotseka+ kwa masiku ogwira ntchito 6.+ Pa tsiku la sabata, ndi pa tsiku lokhala mwezi chipatacho chizitsegulidwa.+
46 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chipata choyang’ana kum’mawa cha bwalo lamkati+ chizikhala chotseka+ kwa masiku ogwira ntchito 6.+ Pa tsiku la sabata, ndi pa tsiku lokhala mwezi chipatacho chizitsegulidwa.+