Ezekieli 44:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Akafuna kupita kubwalo lakunja kumene kuli anthu, azivula zovala zawo zimene anavala potumikira.+ Aziika zovalazo m’zipinda zopatulika zodyeramo+ ndipo azivala zovala zina kuti asayeretse anthu ndi zovala zawozo.+
19 Akafuna kupita kubwalo lakunja kumene kuli anthu, azivula zovala zawo zimene anavala potumikira.+ Aziika zovalazo m’zipinda zopatulika zodyeramo+ ndipo azivala zovala zina kuti asayeretse anthu ndi zovala zawozo.+