Miyambo 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Maere amaponyedwa pamwendo,+ koma zonse zimene maerewo amasonyeza zimachokera kwa Yehova.+ Ezekieli 48:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Anthu inu mugawe dziko limeneli pakati pa mafuko onse a Isiraeli kuti likhale cholowa chawo+ ndi magawo awo,”+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
29 “Anthu inu mugawe dziko limeneli pakati pa mafuko onse a Isiraeli kuti likhale cholowa chawo+ ndi magawo awo,”+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.