1 Samueli 14:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno Sauli anauza Yehova kuti: “Mulungu wa Isiraeli inu, tiyankheni kudzera mwa Tumimu!”+ Atatero, Tumimuyo analoza kwa Yonatani ndi Sauli, ndipo anthuwo anachoka.+ Machitidwe 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo anapemphera kuti: “Ambuye wathu Yehova, inu amene mumadziwa mitima ya anthu onse,+ tisonyezeni amene inu mwamusankha mwa amuna awiriwa,
41 Ndiyeno Sauli anauza Yehova kuti: “Mulungu wa Isiraeli inu, tiyankheni kudzera mwa Tumimu!”+ Atatero, Tumimuyo analoza kwa Yonatani ndi Sauli, ndipo anthuwo anachoka.+
24 Ndipo anapemphera kuti: “Ambuye wathu Yehova, inu amene mumadziwa mitima ya anthu onse,+ tisonyezeni amene inu mwamusankha mwa amuna awiriwa,