Ezekieli 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhata yamaluwa ya tsoka ibwera kwa inu anthu okhala m’dzikoli. Nthawi ikwana. Tsikulo layandikira.+ M’dzikoli muli chisokonezo, osati phokoso lachisangalalo lomveka m’mapiri.
7 Nkhata yamaluwa ya tsoka ibwera kwa inu anthu okhala m’dzikoli. Nthawi ikwana. Tsikulo layandikira.+ M’dzikoli muli chisokonezo, osati phokoso lachisangalalo lomveka m’mapiri.