Yeremiya 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzawamwaza pamaso pa adani awo ngati mmene mphepo yochokera kum’mawa imamwazira fumbi.+ Sindidzawaonetsa nkhope yanga,+ koma ndidzawafulatira pa tsiku la tsoka lawo.”
17 Ndidzawamwaza pamaso pa adani awo ngati mmene mphepo yochokera kum’mawa imamwazira fumbi.+ Sindidzawaonetsa nkhope yanga,+ koma ndidzawafulatira pa tsiku la tsoka lawo.”