Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kenako Yehova anatsika mumtambo+ n’kulankhula naye.+ Anatengako gawo lina la mzimu+ umene unali pa Mose n’kuuika pa aliyense wa akulu 70 amenewo. Ndipo mzimuwo utangokhala pa iwo, anayamba kuchita zinthu ngati aneneri, koma sanadzachitenso kachiwiri.+

  • 1 Samueli 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pamenepo mzimu+ wa Yehova uyamba kugwira ntchito pa iwe, moti iweyo uyamba kulankhula monga mneneri+ pamodzi ndi aneneriwo, ndiponso usinthika kukhala wina.

  • Ezekieli 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Atayamba kulankhula nane, mzimu unalowa mwa ine+ ndipo unandiimiritsa kuti ndimvetsere yemwe anali kulankhula ndi ineyo.+

  • Ezekieli 3:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kenako mzimu unalowa mwa ine+ n’kundiimiritsa,+ ndipo Mulungu anayamba kulankhula nane, kuti:

      “Pita ukadzitsekere m’nyumba mwako.

  • Mika 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma ine ndili ndi mphamvu zochuluka chifukwa cha mzimu wa Yehova. Ndine wokonzeka kuchita zachilungamo ndi kusonyeza mphamvu+ kuti ndiuze mbadwa za Yakobo za kupanduka kwawo, komanso kuti ndiuze Isiraeli za tchimo lake.+

  • 2 Petulo 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena