Yeremiya 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu amene akuwauza maulosi awowo, mitembo yawo idzatayidwa m’misewu ya Yerusalemu chifukwa cha njala ndi lupanga. Sipadzakhala wowaika m’manda, iwowo, akazi awo, ana awo aamuna ndi ana awo aakazi+ chifukwa ndidzawatsanulira tsoka pamutu pawo.’+
16 Anthu amene akuwauza maulosi awowo, mitembo yawo idzatayidwa m’misewu ya Yerusalemu chifukwa cha njala ndi lupanga. Sipadzakhala wowaika m’manda, iwowo, akazi awo, ana awo aamuna ndi ana awo aakazi+ chifukwa ndidzawatsanulira tsoka pamutu pawo.’+