Yeremiya 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Monga mmene mbala imachitira manyazi ikagwidwa, anthu a m’nyumba ya Isiraeli nawonso achita manyazi,+ iwowo, mafumu awo, akalonga awo, ansembe awo ndiponso aneneri awo.+ Ezekieli 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino.+ Mudzanyansidwa ndi zochita zanu, zolakwa zanu ndi zinthu zonyansa zimene munachita.+
26 “Monga mmene mbala imachitira manyazi ikagwidwa, anthu a m’nyumba ya Isiraeli nawonso achita manyazi,+ iwowo, mafumu awo, akalonga awo, ansembe awo ndiponso aneneri awo.+
31 Choncho mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino.+ Mudzanyansidwa ndi zochita zanu, zolakwa zanu ndi zinthu zonyansa zimene munachita.+