Oweruza 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Samisoni anawauza kuti: “Ndiloleni ndikuphereni mwambi.+ Ngati mundiuza tanthauzo lake, m’masiku 7+ a phwandoli, ndidzakupatsani malaya 30 amkati ndi zovala zina 30.+ Miyambo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 kuti azitha kumvetsa mwambi ndi mawu ozunguza mutu,+ mawu a anthu anzeru+ ndi mikuluwiko yawo.+
12 Kenako Samisoni anawauza kuti: “Ndiloleni ndikuphereni mwambi.+ Ngati mundiuza tanthauzo lake, m’masiku 7+ a phwandoli, ndidzakupatsani malaya 30 amkati ndi zovala zina 30.+