Deuteronomo 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Uzitsatira chilungamo.+ Ndithudi uzitsatira chilungamo kuti ukhale ndi moyo ndi kukatengadi dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+ Ezekieli 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ngati akuyendabe m’malamulo anga+ ndi kusunga zigamulo zanga kuti azichita mogwirizana ndi choonadi,+ ndiye kuti munthu wotero ndi wolungama.+ Ndithu adzakhalabe ndi moyo,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Aroma 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pajatu Mose analemba kuti munthu wochita chilungamo cha m’Chilamulo adzakhala ndi moyo chifukwa cha chilungamo chimenecho.+
20 Uzitsatira chilungamo.+ Ndithudi uzitsatira chilungamo kuti ukhale ndi moyo ndi kukatengadi dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+
9 ngati akuyendabe m’malamulo anga+ ndi kusunga zigamulo zanga kuti azichita mogwirizana ndi choonadi,+ ndiye kuti munthu wotero ndi wolungama.+ Ndithu adzakhalabe ndi moyo,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
5 Pajatu Mose analemba kuti munthu wochita chilungamo cha m’Chilamulo adzakhala ndi moyo chifukwa cha chilungamo chimenecho.+