Salimo 92:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuti alengeze kuti Yehova ndi wolungama.+Iye ndi Thanthwe langa,+ ndipo sachita zosalungama.+ Miyambo 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kupusa kwa munthu wochokera kufumbi n’kumene kumapotoza njira yake,+ choncho mtima wake umakwiyira Yehova.+
3 Kupusa kwa munthu wochokera kufumbi n’kumene kumapotoza njira yake,+ choncho mtima wake umakwiyira Yehova.+