Ezekieli 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wafanana ndi Msuri. Wafanana ndi mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,+ wanthambi zikuluzikulu zokongola,+ wanthambi za masamba ambiri zopereka mthunzi, mtengo wautali kwambiri+ umene nsonga yake inafika m’mitambo.+ Danieli 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mtengowo unakula ndipo unakhala wamphamvu kwambiri. Unatalika mpaka kufika kumwamba ndipo unali kuonekera ngakhale kumalekezero a dziko lonse lapansi.+
3 Wafanana ndi Msuri. Wafanana ndi mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,+ wanthambi zikuluzikulu zokongola,+ wanthambi za masamba ambiri zopereka mthunzi, mtengo wautali kwambiri+ umene nsonga yake inafika m’mitambo.+
11 Mtengowo unakula ndipo unakhala wamphamvu kwambiri. Unatalika mpaka kufika kumwamba ndipo unali kuonekera ngakhale kumalekezero a dziko lonse lapansi.+