2 Samueli 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 N’chifukwa chake ndinudi wokwezeka,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Ngakhale kuti tamva za milungu ina yambirimbiri, palibe Mulungu wina+ koma inu nokha.+ Salimo 96:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Yehova ndi wamkulu+ ndi woyenera kutamandidwa kwambiri.Iye ndi wochititsa mantha kuposa milungu ina yonse.+ Salimo 145:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Ndipo ukulu wake ndi wosasanthulika.+ Yeremiya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+
22 N’chifukwa chake ndinudi wokwezeka,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Ngakhale kuti tamva za milungu ina yambirimbiri, palibe Mulungu wina+ koma inu nokha.+
4 Pakuti Yehova ndi wamkulu+ ndi woyenera kutamandidwa kwambiri.Iye ndi wochititsa mantha kuposa milungu ina yonse.+
18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+