2 Samueli 18:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma mfumu inafunsa Mkusiyo kuti: “Kodi mnyamatayo Abisalomu ali bwino?” Poyankha Mkusiyo anati: “Adani anu mbuyanga mfumu ndi anthu onse ofuna kukuchitirani zoipa akhale ngati mnyamatayo.”+
32 Koma mfumu inafunsa Mkusiyo kuti: “Kodi mnyamatayo Abisalomu ali bwino?” Poyankha Mkusiyo anati: “Adani anu mbuyanga mfumu ndi anthu onse ofuna kukuchitirani zoipa akhale ngati mnyamatayo.”+