Danieli 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuwonjezera pamenepo, mfumu inalamulanso kuti tsiku lililonse iwo aziwapatsa zakudya zabwino+ za mfumu ndi vinyo wa mfumu. Inalamulanso kuti awasamalire kwa zaka zitatu ndipo zaka zimenezi zikadzatha, akayambe kutumikira mfumu.
5 Kuwonjezera pamenepo, mfumu inalamulanso kuti tsiku lililonse iwo aziwapatsa zakudya zabwino+ za mfumu ndi vinyo wa mfumu. Inalamulanso kuti awasamalire kwa zaka zitatu ndipo zaka zimenezi zikadzatha, akayambe kutumikira mfumu.