-
2 Mbiri 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 (Pakuti Solomo anapanga nsanja+ yamkuwa n’kuiika pakati pa bwalo lamkati.+ Nsanjayo inali yaikulu mikono isanu m’litali, mikono isanu m’lifupi, ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba inali yaitali mikono itatu. Iye anaimirira pansanjayo.) Atatero anagwada+ patsogolo pa mpingo wonse wa Isiraeli. Kenako anatambasula manja ake n’kuwakweza kumwamba.+
-
-
Luka 22:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Iye analekana nawo ndi kuyenda kamtunda, kutalika kwake ngati pamene pangagwere mwala munthu atauponya. Kumeneko anagwada ndi kuyamba kupemphera,
-