Mateyu 27:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Choncho anapita ndi kukakhwimitsa chitetezo pamandawo mwa kutseka kwambiri mandawo ndi chimwala*+ n’kuikapo asilikali olondera. Machitidwe 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Atamugwira, anamutsekera m’ndende+ ndipo anamupereka m’manja mwa magulu anayi a asilikali, kuti azisinthana pomulondera. Gulu lililonse linali ndi asilikali anayi. Cholinga cha Herode chinali chakuti adzamuonetse kwa anthu pambuyo pa pasika.+
66 Choncho anapita ndi kukakhwimitsa chitetezo pamandawo mwa kutseka kwambiri mandawo ndi chimwala*+ n’kuikapo asilikali olondera.
4 Atamugwira, anamutsekera m’ndende+ ndipo anamupereka m’manja mwa magulu anayi a asilikali, kuti azisinthana pomulondera. Gulu lililonse linali ndi asilikali anayi. Cholinga cha Herode chinali chakuti adzamuonetse kwa anthu pambuyo pa pasika.+