Danieli 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Imodzi mwa nyangazi inatulutsa nyanga ina yaing’ono+ imene inayamba kukula kwambiri moloza kum’mwera, moloza kotulukira dzuwa ndiponso moloza ku Dziko Lokongola.+
9 Imodzi mwa nyangazi inatulutsa nyanga ina yaing’ono+ imene inayamba kukula kwambiri moloza kum’mwera, moloza kotulukira dzuwa ndiponso moloza ku Dziko Lokongola.+