Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+ Yesaya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’tsiku limenelo, chinthu chimene Yehova adzachiphukitse+ chidzakhala chokongoletsera ndi chaulemerero.+ Zipatso za m’dzikolo zidzakhala zonyaditsa+ ndi zokongola kwa Aisiraeli amene adzapulumuke.+ Yesaya 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu adzakhala ngati chisoti chokongoletsera+ ndiponso ngati nkhata yamaluwa yokongola+ kwa anthu ake otsala.+ Ezekieli 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa tsiku limenelo ndinakweza dzanja langa+ powalumbirira kuti ndidzawatulutsa m’dziko la Iguputo kupita nawo kudziko limene ndinaliyendera kuti iwo akakhalemo, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Linali dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse.+ Danieli 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mfumu yobwera kudzamenyana nayo* idzachita zofuna zake, ndipo palibe adzaime pamaso pake. Mfumuyo idzaimirira m’Dziko Lokongola,+ ndipo idzapha anthu ambiri.+ Danieli 11:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndipo idzamanga mahema okhala ngati nyumba yachifumu pakati pa nyanja yaikulu ndi phiri lopatulika la Dziko Lokongola.+ Ndiyeno iyo idzafika kumapeto a moyo wake+ ndipo sipadzapezeka woithandiza.+
2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+
2 M’tsiku limenelo, chinthu chimene Yehova adzachiphukitse+ chidzakhala chokongoletsera ndi chaulemerero.+ Zipatso za m’dzikolo zidzakhala zonyaditsa+ ndi zokongola kwa Aisiraeli amene adzapulumuke.+
5 M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu adzakhala ngati chisoti chokongoletsera+ ndiponso ngati nkhata yamaluwa yokongola+ kwa anthu ake otsala.+
6 Pa tsiku limenelo ndinakweza dzanja langa+ powalumbirira kuti ndidzawatulutsa m’dziko la Iguputo kupita nawo kudziko limene ndinaliyendera kuti iwo akakhalemo, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Linali dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse.+
16 Mfumu yobwera kudzamenyana nayo* idzachita zofuna zake, ndipo palibe adzaime pamaso pake. Mfumuyo idzaimirira m’Dziko Lokongola,+ ndipo idzapha anthu ambiri.+
45 Ndipo idzamanga mahema okhala ngati nyumba yachifumu pakati pa nyanja yaikulu ndi phiri lopatulika la Dziko Lokongola.+ Ndiyeno iyo idzafika kumapeto a moyo wake+ ndipo sipadzapezeka woithandiza.+