Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando+ akalonga ndi atumiki ake onse, akuluakulu a asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka+ ndi akalonga a m’zigawo za ufumu wake.+

  • Yesaya 44:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndine amene ndikunena za Koresi+ kuti, ‘Iye ndi m’busa wanga ndipo adzakwaniritsa bwinobwino zonse zimene ndikufuna,’+ ngakhale zimene ndanena zokhudza Yerusalemu zakuti, ‘Adzamangidwanso,’ ndi zokhudza kachisi zakuti, ‘Maziko ako adzamangidwa.’”+

  • Danieli 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano ndikufotokozera choonadi:+

      “Mu ufumu wa Perisiya+ mudzauka mafumu atatu, ndipo mfumu yachinayi+ idzasonkhanitsa chuma chambiri kuposa ena onsewa.+ Ndipo ikadzangokhala yamphamvu chifukwa cha chuma chakecho idzaukira ufumu wa Girisi ndi mphamvu zake zonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena