Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 11:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiyeno padzauka magulu ankhondo* otuluka mwa iye. Maguluwo adzaipitsa malo opatulika+ amene ndi malo okhala ndi mpanda wolimba kwambiri, ndipo adzachotsa nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse.+

      “Iwo adzaika pamalowo chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko.+

  • 1 Akorinto 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ngati munthu aliyense wawononga kachisi wa Mulungu, Mulungu adzawononganso munthu ameneyo,+ pakuti kachisi wa Mulungu ndi woyera,+ ndipo kachisiyo+ ndinuyo.+

  • Chivumbulutso 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “‘Wopambana pa nkhondo, ndidzamuika kukhala mzati+ m’kachisi+ wa Mulungu wanga,+ ndipo sadzachokamonso. Ndidzamulemba dzina la Mulungu wanga, ndiponso dzina la mzinda wa Mulungu wanga, Yerusalemu watsopano,+ wotsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu wanga. Ndidzamulembanso dzina langa latsopano.+

  • Chivumbulutso 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Koma bwalo lakunja+ kwa nyumba yopatulika ya pakachisi ulisiye, usaliyeze m’pang’ono pomwe chifukwa laperekedwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo iwo adzapondaponda mzinda woyera+ kwa miyezi 42.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena