Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Kuchokera pa nthawi imene nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zidzachotsedwa,+ ndiponso pamene chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko chidzaikidwa, padzapita masiku 1,290.

  • Mateyu 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Choncho, mukadzaona chinthu chonyansa+ chowononga chimene chinanenedwa kudzera mwa mneneri Danieli chitaimirira m’malo oyera,+ (wowerenga adzazindikire,)

  • Chivumbulutso 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndipo chinaloledwa kupereka mpweya ku chifaniziro cha chilombo chija, kuti chifaniziro cha chilombocho chithe kulankhula, ndi kuchititsa kuti onse amene mwa njira iliyonse salambira chifaniziro+ cha chilombocho, aphedwe.

  • Chivumbulutso 17:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chilombo chimene waona, chinalipo,+ tsopano palibe, komabe chili pafupi kutuluka kuphompho,+ ndipo chidzapita ku chiwonongeko. Anthu okhala padziko lapansi akaona kuti chilombocho chinalipo, tsopano palibe, komabe chidzakhalapo, adzadabwa kwambiri pochita nacho chidwi. Koma mayina awo sanalembedwe mumpukutu wa moyo+ kuyambira pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena