Ekisodo 29:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku nthawi zonse.+ Numeri 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+ Salimo 119:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndidzasunga chilamulo chanu nthawi zonse,+Mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Danieli 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha uchimo,+ khamulo ndi nsembe yoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zinaperekedwa kwa nyangayo,+ ndipo inali kugwetsera choonadi+ pansi.+ Nyangayo inali kuchita zofuna zake ndipo inapambana.+ Danieli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Kuchokera pa nthawi imene nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zidzachotsedwa,+ ndiponso pamene chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko chidzaikidwa, padzapita masiku 1,290.
38 “Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku nthawi zonse.+
3 “Uwauze kuti, ‘Muzipereka kwa Yehova nsembe yotentha ndi moto motere: Tsiku lililonse muzipereka nsembe yopsereza ya ana a nkhosa awiri amphongo, achaka chimodzi ndi opanda chilema.+
12 Chifukwa cha uchimo,+ khamulo ndi nsembe yoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zinaperekedwa kwa nyangayo,+ ndipo inali kugwetsera choonadi+ pansi.+ Nyangayo inali kuchita zofuna zake ndipo inapambana.+
11 “Kuchokera pa nthawi imene nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zidzachotsedwa,+ ndiponso pamene chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko chidzaikidwa, padzapita masiku 1,290.