Danieli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Kuchokera pa nthawi imene nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zidzachotsedwa,+ ndiponso pamene chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko chidzaikidwa, padzapita masiku 1,290. Mateyu 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Choncho, mukadzaona chinthu chonyansa+ chowononga chimene chinanenedwa kudzera mwa mneneri Danieli chitaimirira m’malo oyera,+ (wowerenga adzazindikire,) Maliko 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Koma mukadzaona chinthu chonyansa+ chosakaza+ chitaimirira pamene sichiyenera kuima (wowerenga adzazindikire),+ pamenepo amene ali mu Yudeya adzayambe kuthawira kumapiri.+
11 “Kuchokera pa nthawi imene nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zidzachotsedwa,+ ndiponso pamene chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko chidzaikidwa, padzapita masiku 1,290.
15 “Choncho, mukadzaona chinthu chonyansa+ chowononga chimene chinanenedwa kudzera mwa mneneri Danieli chitaimirira m’malo oyera,+ (wowerenga adzazindikire,)
14 “Koma mukadzaona chinthu chonyansa+ chosakaza+ chitaimirira pamene sichiyenera kuima (wowerenga adzazindikire),+ pamenepo amene ali mu Yudeya adzayambe kuthawira kumapiri.+