31 Ndiyeno padzauka magulu ankhondo otuluka mwa iye. Maguluwo adzaipitsa malo opatulika+ amene ndi malo okhala ndi mpanda wolimba kwambiri, ndipo adzachotsa nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse.+
“Iwo adzaika pamalowo chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko.+