Danieli 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno ndinayamba kumva mawu ake. Pamene ndinali kumva mawuwo ndinagona pansi+ chafufumimba n’kugona tulo tofa nato.+
9 Ndiyeno ndinayamba kumva mawu ake. Pamene ndinali kumva mawuwo ndinagona pansi+ chafufumimba n’kugona tulo tofa nato.+