Danieli 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene anali kulankhula nane ndinagona pansi chafufumimba n’kugona tulo tofa nato.+ Ndiyeno iye anandigwira ndi kundiimiritsa pamalo pomwe ndinaima paja.+
18 Pamene anali kulankhula nane ndinagona pansi chafufumimba n’kugona tulo tofa nato.+ Ndiyeno iye anandigwira ndi kundiimiritsa pamalo pomwe ndinaima paja.+