Danieli 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Mafumu awiri amenewa adzakhala ndi mtima wofuna kuchita zoipa, ndipo azidzalankhula bodza+ patebulo limodzi.+ Koma zolinga zawo zonse sizidzatheka+ chifukwa nthawi yamapeto sinakwane.+ Mateyu 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atakhala pansi m’phiri la Maolivi, ophunzira anafika kwa iye mwamseri ndi kunena kuti: “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino chidzakhala chiyani?”+
27 “Mafumu awiri amenewa adzakhala ndi mtima wofuna kuchita zoipa, ndipo azidzalankhula bodza+ patebulo limodzi.+ Koma zolinga zawo zonse sizidzatheka+ chifukwa nthawi yamapeto sinakwane.+
3 Atakhala pansi m’phiri la Maolivi, ophunzira anafika kwa iye mwamseri ndi kunena kuti: “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino chidzakhala chiyani?”+