Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,

      Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+

      Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+

      Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+

  • Salimo 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Yehova adzadula milomo yonse yolankhula zachinyengo

      Ndi lilime lolankhula modzikuza.+

  • Danieli 8:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Chifukwa cha kuzindikira kwake idzathadi kugwiritsa ntchito chinyengo.+ Idzadzitukumula kwambiri mumtima mwake,+ ndipo idzawononga anthu ambiri pa nthawi imene zinthu zikuiyendera bwino.+ Mfumuyo idzalimbana ndi Kalonga wa akalonga,+ ndipo idzathyoledwa koma osati ndi dzanja la munthu.+

  • Chivumbulutso 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chilombocho chinapatsidwa pakamwa polankhula zinthu zodzitukumula+ ndi zonyoza.+ Chinapatsidwanso mphamvu yochita ulamuliro kwa miyezi 42.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena