Danieli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ndinatsala ndekha ndipo ndinaona masomphenya odabwitsawa. Pamenepo mphamvu zonse zinandithera, ndipo maonekedwe olemekezeka a nkhope yanga anasintha kwambiri n’kukhala omvetsa chisoni, moti ndinalibenso mphamvu.+
8 Choncho ndinatsala ndekha ndipo ndinaona masomphenya odabwitsawa. Pamenepo mphamvu zonse zinandithera, ndipo maonekedwe olemekezeka a nkhope yanga anasintha kwambiri n’kukhala omvetsa chisoni, moti ndinalibenso mphamvu.+