-
Habakuku 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Nditamva mawu ake, m’mimba mwanga munayamba kubwadamuka ndipo milomo yanga inanjenjemera. Mafupa anga anayamba kuwola+ ndipo ndinanthunthumira chifukwa cha mmene zinthu zinalili. Choncho ndidzayembekezera mofatsa tsiku la nsautso.+ Tsiku limeneli lidzabwera kwa anthu+ ngati mmene munthu amabwerera kwa adani ake kuti awaukire.
-