Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 10:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Inde, adzakutengerani kwa abwanamkubwa ndi mafumu+ chifukwa cha ine, kuti ukhale umboni+ kwa iwo ndi kwa anthu a mitundu ina.

  • Mateyu 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+

  • Yohane 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu adzakuchotsani m’sunagoge.+ Ndipo nthawi ikubwera pamene aliyense wakupha inu adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.+

  • Chivumbulutso 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi+ adzapitiriza kuponya m’ndende ena a inu, kuti muyesedwe mpaka pamapeto,+ ndipo mudzakhala m’masautso+ masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa,+ ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+

  • Chivumbulutso 12:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndipo chinjokacho chinakwiya ndi mkazi uja,+ moti chinapita kukachita nkhondo ndi otsala a mbewu yake, amene amasunga malamulo a Mulungu, amenenso ali ndi ntchito yochitira umboni+ za Yesu.

  • Chivumbulutso 16:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 pakuti iwo anakhetsa magazi a oyera ndi a aneneri.+ Ndipo inu mwawapatsa magazi+ kuti amwe, ndipo n’zowayenereradi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena