2 “Ndani adzapirire pa tsiku limene adzabwere?+ Ndipo ndani adzaime chilili iye akadzaonekera?+ Iye adzakhala ngati moto wa woyenga zitsulo+ komanso ngati sopo+ wa ochapa zovala.+
3 Atakhala pansi m’phiri la Maolivi, ophunzira anafika kwa iye mwamseri ndi kunena kuti: “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino chidzakhala chiyani?”+