Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+ Mateyu 24:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamenepo adzam’patsa chilango choopsa+ ndipo adzam’ponya kumene kuli anthu onyenga. Kumeneko ndiye kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.+ Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+
7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
51 Pamenepo adzam’patsa chilango choopsa+ ndipo adzam’ponya kumene kuli anthu onyenga. Kumeneko ndiye kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.+