Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 97:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kuwala kwaunikira wolungama,+

      Ndipo anthu owongoka mtima akusangalala.+

  • Yesaya 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Sizidzavulazana+ kapena kuwonongana m’phiri langa lonse loyera,+ chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa Yehova ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+

  • Yesaya 58:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 mukapatsa munthu wanjala zinthu zimene inuyo mumakonda,+ ndiponso mukakhutiritsa munthu amene akusautsidwa, kuunika kwanu kudzawala kuti ngwee! mu mdima, ndipo mdima wanu udzakhala ngati masana dzuwa likakhala paliwombo.+

  • Chivumbulutso 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mzimu+ ndi mkwatibwi+ akunenabe kuti: “Bwera!” Aliyense wakumva anene kuti: “Bwera!”+ Aliyense wakumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi a moyo kwaulere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena