Salimo 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaonetsa poyera kulungama kwako kuti kuunike ngati kuwala,+Adzaonetsa poyera chilungamo chako kuti chiwale ngati usana.+ Yesaya 58:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Mukatero kuwala kwanu kudzaonekera ngati m’bandakucha,+ ndipo mudzachira mofulumira kwambiri.+ Chilungamo chanu chizidzayenda patsogolo panu,+ ndipo ulemerero wa Yehova uzidzalondera kumbuyo kwanu.+
6 Iye adzaonetsa poyera kulungama kwako kuti kuunike ngati kuwala,+Adzaonetsa poyera chilungamo chako kuti chiwale ngati usana.+
8 “Mukatero kuwala kwanu kudzaonekera ngati m’bandakucha,+ ndipo mudzachira mofulumira kwambiri.+ Chilungamo chanu chizidzayenda patsogolo panu,+ ndipo ulemerero wa Yehova uzidzalondera kumbuyo kwanu.+