Danieli 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Thupi lake linali ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inali yowala ngati mphezi,+ maso ake anali kuoneka ngati miyuni yamoto,+ manja ake ndi mapazi ake zinali kuoneka ngati mkuwa wonyezimira,+ ndipo mawu ake anali kumveka ngati khamu la anthu. Danieli 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno winawake wamaonekedwe ofanana ndi ana a anthu anakhudza milomo yanga.+ Atatero, ndinayamba kulankhula,+ ndipo ndinauza amene anali ataimirira patsogolo panga uja kuti: “Mbuyanga,+ ine ndinayamba kunjenjemera chifukwa cha zimene ndaona ndipo mphamvu zandithera.+
6 Thupi lake linali ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inali yowala ngati mphezi,+ maso ake anali kuoneka ngati miyuni yamoto,+ manja ake ndi mapazi ake zinali kuoneka ngati mkuwa wonyezimira,+ ndipo mawu ake anali kumveka ngati khamu la anthu.
16 Ndiyeno winawake wamaonekedwe ofanana ndi ana a anthu anakhudza milomo yanga.+ Atatero, ndinayamba kulankhula,+ ndipo ndinauza amene anali ataimirira patsogolo panga uja kuti: “Mbuyanga,+ ine ndinayamba kunjenjemera chifukwa cha zimene ndaona ndipo mphamvu zandithera.+