Salimo 74:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, kodi mdani adzakuchitirani mopanda ulemu kufikira liti?+Kodi mdani adzanyoza dzina lanu kwamuyaya?+ Chivumbulutso 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera kufikira liti, Inu Ambuye Wamkulu Koposa,+ woyera ndi woona,+ osaweruza+ ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi+ athu?”
10 Inu Mulungu, kodi mdani adzakuchitirani mopanda ulemu kufikira liti?+Kodi mdani adzanyoza dzina lanu kwamuyaya?+
10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera kufikira liti, Inu Ambuye Wamkulu Koposa,+ woyera ndi woona,+ osaweruza+ ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi+ athu?”