Deuteronomo 32:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adzalefuka ndi njala+ ndi kuwonongeka ndi matenda otentha thupi koopsa,+Ndi chiwonongeko chowawa.+Ndidzawatumizira zilombo za mano ataliatali,+Pamodzi ndi njoka zapoizoni za m’fumbi.+ 2 Mafumu 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Elisa anauza mayi amene anamuukitsira mwana uja,+ kuti: “Nyamuka, iwe ndi banja lako, ukakhale monga mlendo kulikonse kumene ungakakhale,+ chifukwa Yehova abweretsa njala.+ Njalayo idzatenga zaka 7.”+
24 Adzalefuka ndi njala+ ndi kuwonongeka ndi matenda otentha thupi koopsa,+Ndi chiwonongeko chowawa.+Ndidzawatumizira zilombo za mano ataliatali,+Pamodzi ndi njoka zapoizoni za m’fumbi.+
8 Tsopano Elisa anauza mayi amene anamuukitsira mwana uja,+ kuti: “Nyamuka, iwe ndi banja lako, ukakhale monga mlendo kulikonse kumene ungakakhale,+ chifukwa Yehova abweretsa njala.+ Njalayo idzatenga zaka 7.”+