Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 11:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Wofunafuna kuchitira ena zabwino, amafunafuna kuvomerezedwa ndi Mulungu.*+ Koma wofunafuna kuchita zoipa, zoipazo zidzam’bwerera.+

  • Yesaya 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Sambani,+ dziyeretseni.+ Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.+ Lekani kuchita zoipa.+

  • Mika 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+

  • Aroma 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Moyo wosatha kwa anthu amene popirira m’ntchito yabwino akuyesetsa kupeza ulemerero, ulemu ndi moyo wosakhoza kuwonongeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena