Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+

      Ndipo adzamva chisoni chifukwa cha atumiki ake,+

      Chifukwa adzaona kuti thandizo lawachokera.

      Adzaona kuti pangokhala munthu wonyozeka ndi wopanda pake.

  • Salimo 106:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+

      Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+

  • Hoseya 11:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Kodi ndikusiyirenji iwe Efuraimu?+ Kodi ndikuperekerenji kwa adani iwe Isiraeli?+ Kodi ndikusandutsirenji ngati Adima?+ Kodi ndikuchitirenji zofanana ndi zimene ndinachitira Zeboyimu?+ Mtima wanga wasintha+ ndipo pa nthawi imodzimodziyo wadzaza ndi chisoni.

  • Yona 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Mulungu woona anaona ntchito zawo.+ Anaona kuti alapa ndi kusiya njira zawo zoipa.+ Choncho, Mulungu woona anasintha maganizo ake+ pa tsoka limene ananena kuti awabweretsera, moti sanawabweretsere.+

  • Yakobo 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena