Mateyu 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi n’kosaloleka kuchita zimene ndikufuna ndi zinthu zanga? Kapena diso lako lachita njiru+ chifukwa chakuti ndine wabwino?’+ Aroma 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+ Yakobo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kapena mukuyesa kuti lemba limanena pachabe kuti: “Mzimu umene uli mwa ife uli ndi chizolowezi cholakalaka zinthu zosiyanasiyana”?+
15 Kodi n’kosaloleka kuchita zimene ndikufuna ndi zinthu zanga? Kapena diso lako lachita njiru+ chifukwa chakuti ndine wabwino?’+
16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+
5 Kapena mukuyesa kuti lemba limanena pachabe kuti: “Mzimu umene uli mwa ife uli ndi chizolowezi cholakalaka zinthu zosiyanasiyana”?+