2 Mbiri 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anayamba kuphunzitsa+ mu Yuda pogwiritsira ntchito buku la chilamulo cha Yehova.+ Ankayendayenda m’mizinda yonse ya Yuda n’kumaphunzitsa anthu. Ezekieli 44:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo aziimirira pa mlandu ndi kuweruza.+ Aziweruza motsatira zigamulo zanga.+ Azisunga malamulo ndi malangizo anga okhudza zikondwerero zanga zonse,+ ndipo aziyeretsa masabata anga.+
9 Iwo anayamba kuphunzitsa+ mu Yuda pogwiritsira ntchito buku la chilamulo cha Yehova.+ Ankayendayenda m’mizinda yonse ya Yuda n’kumaphunzitsa anthu.
24 Iwo aziimirira pa mlandu ndi kuweruza.+ Aziweruza motsatira zigamulo zanga.+ Azisunga malamulo ndi malangizo anga okhudza zikondwerero zanga zonse,+ ndipo aziyeretsa masabata anga.+