Mateyu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atadziwa zimenezi, Yesu anatuluka mmenemo. Anthu ambiri anam’tsatira ndipo iye anawachiritsa onsewo,+ Mateyu 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yesu atatsika m’ngalawayo anaona khamu lalikulu la anthu, ndipo anawamvera chisoni,+ ndi kuwachiritsira anthu awo odwala.+ Mateyu 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako anthu ochuluka anakhamukira kwa iye. Anabwera ndi anthu olumala, othyoka ziwalo, akhungu, osalankhula, ndi ena ambiri osiyanasiyana, moti anawakhazika pamapazi ake mochita ngati akum’ponyera, ndipo anawachiritsa onsewo.+ Luka 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mbiri yake inali kufalikira kwambiri, ndipo makamu a anthu anali kusonkhana pamodzi kudzamumvetsera ndi kudzachiritsidwa matenda awo.+
15 Atadziwa zimenezi, Yesu anatuluka mmenemo. Anthu ambiri anam’tsatira ndipo iye anawachiritsa onsewo,+
14 Tsopano Yesu atatsika m’ngalawayo anaona khamu lalikulu la anthu, ndipo anawamvera chisoni,+ ndi kuwachiritsira anthu awo odwala.+
30 Kenako anthu ochuluka anakhamukira kwa iye. Anabwera ndi anthu olumala, othyoka ziwalo, akhungu, osalankhula, ndi ena ambiri osiyanasiyana, moti anawakhazika pamapazi ake mochita ngati akum’ponyera, ndipo anawachiritsa onsewo.+
15 Koma mbiri yake inali kufalikira kwambiri, ndipo makamu a anthu anali kusonkhana pamodzi kudzamumvetsera ndi kudzachiritsidwa matenda awo.+