Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 40:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+

  • Mateyu 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mneneri Yesaya ananenera za iyeyu+ m’mawu awa: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani+ njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.’”

  • Luka 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Komanso, adzatsogola monga kalambulabwalo wa Mulungu ali ndi mzimu ndi mphamvu ngati za Eliya.+ Iye adzatembenuza mitima+ ya abambo kuti ikhale ngati ya ana, ndipo osamvera adzawatembenuzira ku nzeru yeniyeni ya anthu olungama. Adzachita izi kuti asonkhanitsire Yehova+ anthu okonzedwa.”+

  • Luka 1:76
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 76 Koma kunena za iwe, mwanawe, udzatchedwa mneneri wa Wam’mwambamwamba, pakuti udzatsogola pamaso pa Yehova kuti ukakonzeretu njira zake.+

  • Luka 7:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Malemba amanena za iyeyu kuti, ‘Taona! Inetu ndikutumiza mthenga wanga choyamba,+ amene adzakukonzera njira.’+

  • Yohane 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Inu nomwe ndinu mboni zanga pamawu amene ndinanena kuti, Ine sindine Khristu,+ koma, ndinatumizidwa monga kalambulabwalo wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena