Yohane 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Inenso sindinali kumudziwa, koma Amene anandituma+ kudzabatiza m’madzi anandiuza kuti, ‘Ukadzaona mzimu ukutsika ndi kukhazikika pa munthu wina, ameneyo ndiye wobatiza ndi mzimu woyera.’+ Machitidwe 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa Yohane anabatizadi ndi madzi, koma pasanathe masiku ambiri mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.”+ Machitidwe 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero ndinakumbukira mawu a Ambuye aja akuti, ‘Yohane anabatiza ndi madzi,+ koma inu mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.’+
33 Inenso sindinali kumudziwa, koma Amene anandituma+ kudzabatiza m’madzi anandiuza kuti, ‘Ukadzaona mzimu ukutsika ndi kukhazikika pa munthu wina, ameneyo ndiye wobatiza ndi mzimu woyera.’+
5 Chifukwa Yohane anabatizadi ndi madzi, koma pasanathe masiku ambiri mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.”+
16 Zitatero ndinakumbukira mawu a Ambuye aja akuti, ‘Yohane anabatiza ndi madzi,+ koma inu mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.’+